1 Samueli 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wang’amba+ ndi kuchotsa ufumu wa Isiraeli kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa mnzako, munthu woyenerera kuposa iwe.+ 1 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taona! Ine ndikudziwa bwino kwambiri kuti mosalephera iweyo udzalamulira monga mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhazikika m’banja lako nthawi zonse. 1 Samueli 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+ Yobu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wolungama akuyendabe panjira yake,+Ndipo wa manja oyera+ akungowonjezeka mphamvu.+
28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wang’amba+ ndi kuchotsa ufumu wa Isiraeli kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa mnzako, munthu woyenerera kuposa iwe.+
20 Taona! Ine ndikudziwa bwino kwambiri kuti mosalephera iweyo udzalamulira monga mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhazikika m’banja lako nthawi zonse.
25 Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Udalitsike mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu ndipo udzapambana ndithu.”+ Pamenepo Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+