Salimo 119:165 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 165 Okonda chilamulo chanu amapeza mtendere wochuluka,+Ndipo palibe chowakhumudwitsa.+ Miyambo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzakutsogolera m’njira ya nzeru.+ Ndidzakuchititsa kuyenda m’njira zowongoka.+