Yobu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kudziko la Uzi+ kunali munthu wina dzina lake Yobu.+ Iye anali munthu wopanda cholakwa,+ wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+ Salimo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amatsitsimula moyo wanga.+Amanditsogolera m’tinjira tachilungamo chifukwa cha dzina lake.+ Yesaya 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+ Malaki 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lamulo la choonadi linali m’kamwa mwake+ ndipo pamilomo pake panalibe zosalungama. Anali kuyenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima,+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira zawo zolakwika.+
1 Kudziko la Uzi+ kunali munthu wina dzina lake Yobu.+ Iye anali munthu wopanda cholakwa,+ wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+
7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+
6 Lamulo la choonadi linali m’kamwa mwake+ ndipo pamilomo pake panalibe zosalungama. Anali kuyenda ndi ine mwamtendere komanso mowongoka mtima,+ ndipo anabweza anthu ambiri panjira zawo zolakwika.+