Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri+ wa anthu ake chifukwa iwe sunasunge zimene Yehova anakulamula.”+

  • 1 Samueli 15:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wang’amba+ ndi kuchotsa ufumu wa Isiraeli kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa mnzako, munthu woyenerera kuposa iwe.+

  • 1 Samueli 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Sauli atamva zimenezi anakwiya kwambiri+ ndipo mawu amenewa anamuipira, moti anayamba kuganiza kuti: “Davide amupatsa masauzande makumimakumi, koma ine angondipatsa masauzande okha. Ndiye kuti kwangotsala kum’patsa ufumuwu basi!”+

  • 1 Samueli 20:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Masiku onse amene mwana wa Jeseyo adzakhala ndi moyo, iweyo ndi ufumu wako sudzakhazikika ayi.+ Choncho tumiza anthu akamugwire ndi kumubweretsa kwa ine, pakuti ayenera kufa ndithu.”+

  • 1 Samueli 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno anamuuza kuti: “Usachite mantha,+ chifukwa dzanja la Sauli bambo anga silikupeza, moti iwe ukhaladi mfumu+ ya Isiraeli, ndipo ine ndidzakhala wachiwiri kwa iwe. Sauli bambo anga akudziwa bwino zimenezi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena