1 Samueli 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Masiku onse amene mwana wa Jeseyo adzakhala ndi moyo, iweyo ndi ufumu wako sudzakhazikika ayi.+ Choncho tumiza anthu akamugwire ndi kumubweretsa kwa ine, pakuti ayenera kufa ndithu.”+ 1 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taona! Ine ndikudziwa bwino kwambiri kuti mosalephera iweyo udzalamulira monga mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhazikika m’banja lako nthawi zonse.
31 Masiku onse amene mwana wa Jeseyo adzakhala ndi moyo, iweyo ndi ufumu wako sudzakhazikika ayi.+ Choncho tumiza anthu akamugwire ndi kumubweretsa kwa ine, pakuti ayenera kufa ndithu.”+
20 Taona! Ine ndikudziwa bwino kwambiri kuti mosalephera iweyo udzalamulira monga mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhazikika m’banja lako nthawi zonse.