1 Mafumu 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo nkhondo inkachitika nthawi zonse pakati pa Rehobowamu ndi Yerobowamu.+ 1 Mafumu 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pa Asa ndi Basa+ mfumu ya Isiraeli, panali kuchitika nkhondo masiku awo onse.