1 Mafumu 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova wati: “Musapite kukamenyana ndi abale anu, ana a Isiraeli.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake, chifukwa zimene zachitikazi, zachitika mwa kufuna kwanga.”’”+ Choncho anamvera mawu a Yehova+ n’kubwerera kwawo malinga ndi mawu a Yehova.+ 1 Mafumu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa Rehobowamu ndi Yerobowamu pankachitika nkhondo masiku onse a moyo wa Rehobowamu.+
24 ‘Yehova wati: “Musapite kukamenyana ndi abale anu, ana a Isiraeli.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake, chifukwa zimene zachitikazi, zachitika mwa kufuna kwanga.”’”+ Choncho anamvera mawu a Yehova+ n’kubwerera kwawo malinga ndi mawu a Yehova.+