2 Mbiri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Yehova wati: “Musapite kukamenyana ndi abale anu.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake, chifukwa zimene zachitikazi, zachitika mwa kufuna kwanga.”’”+ Choncho anamvera mawu a Yehova n’kubwerera, osakamenyana ndi Yerobowamu.+
4 ‘Yehova wati: “Musapite kukamenyana ndi abale anu.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake, chifukwa zimene zachitikazi, zachitika mwa kufuna kwanga.”’”+ Choncho anamvera mawu a Yehova n’kubwerera, osakamenyana ndi Yerobowamu.+