1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+ 2 Mbiri 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo sinamvere anthuwo chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Mulungu woona,+ kuti Yehova akwaniritse mawu ake+ amene analankhula kwa Yerobowamu mwana wa Nebati,+ kudzera mwa Ahiya+ Msilo.+
31 Atatero, anamuuza Yerobowamu kuti: “Tengapo zidutswa 10, pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wati, ‘Ndikung’amba ufumuwu kuuchotsa m’manja mwa Solomo, ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
15 Mfumuyo sinamvere anthuwo chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Mulungu woona,+ kuti Yehova akwaniritse mawu ake+ amene analankhula kwa Yerobowamu mwana wa Nebati,+ kudzera mwa Ahiya+ Msilo.+