29 Kuwonjezera apo, Wolemekezeka wa Isiraeli+ sadzalephera kukwaniritsa mawu ake,+ ndipo sadzadzimva kuti ali ndi mlandu, pakuti Iye si munthu kuti adzimve wamlandu.”+
10 Tsopano dziwani kuti mawu onse a Yehova otsutsa nyumba ya Ahabu+ amene Yehova analankhula, adzakwaniritsidwa.+ Yehova wachita zimene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Eliya.”+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+