Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 15:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+

  • 2 Samueli 15:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma ukabwerera kumzinda ndi kukauza Abisalomu kuti, ‘Inu Mfumu ine ndine mtumiki wanu. Kale ndinali mtumiki wa bambo anu, koma tsopano ndine mtumiki wanu,’+ pamenepo ukanditsutsire+ malangizo a Ahitofeli.

  • Yobu 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kwa Iye amene amalepheretsa zolinga za ochenjera,+

      Mwakuti ntchito imene manja awo amagwira siioneka.

  • Miyambo 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+

  • Miyambo 21:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+

  • Yesaya 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+

  • 1 Akorinto 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti kwa Mulungu nzeru za m’dzikoli n’zopusa,+ chifukwa Malemba amati: “Iye amakola anzeru m’kuchenjera kwawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena