2 Samueli 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndibwereze kunena kuti, Ine ndingatumikire ndani? Kodi sindiyenera kutumikira mwana wake? Monga mmene ndinatumikira bambo anu, ndichitanso chimodzimodzi kwa inu.”+
19 Ndibwereze kunena kuti, Ine ndingatumikire ndani? Kodi sindiyenera kutumikira mwana wake? Monga mmene ndinatumikira bambo anu, ndichitanso chimodzimodzi kwa inu.”+