2 Samueli 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma ukabwerera kumzinda ndi kukauza Abisalomu kuti, ‘Inu Mfumu ine ndine mtumiki wanu. Kale ndinali mtumiki wa bambo anu, koma tsopano ndine mtumiki wanu,’+ pamenepo ukanditsutsire+ malangizo a Ahitofeli. Miyambo 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+
34 Koma ukabwerera kumzinda ndi kukauza Abisalomu kuti, ‘Inu Mfumu ine ndine mtumiki wanu. Kale ndinali mtumiki wa bambo anu, koma tsopano ndine mtumiki wanu,’+ pamenepo ukanditsutsire+ malangizo a Ahitofeli.
15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+