Deuteronomo 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Sihoni mfumu ya Hesiboni sanatilole kudutsa m’dziko lake, chifukwa Yehova Mulungu wanu anamulola kuti akhale wokanika+ ndi kuti aumitse mtima wake. Anatero kuti am’pereke m’manja mwanu monga mmene zilili lero.+ 2 Mbiri 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Amaziya sanamvere, popeza Mulungu woona+ ndi amene anachititsa zimenezi kuti awapereke m’manja mwa adani, chifukwa iwo anafunafuna milungu ya Edomu.+ Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+
30 Koma Sihoni mfumu ya Hesiboni sanatilole kudutsa m’dziko lake, chifukwa Yehova Mulungu wanu anamulola kuti akhale wokanika+ ndi kuti aumitse mtima wake. Anatero kuti am’pereke m’manja mwanu monga mmene zilili lero.+
20 Koma Amaziya sanamvere, popeza Mulungu woona+ ndi amene anachititsa zimenezi kuti awapereke m’manja mwa adani, chifukwa iwo anafunafuna milungu ya Edomu.+