Deuteronomo 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Sihoni mfumu ya Hesiboni sanatilole kudutsa m’dziko lake, chifukwa Yehova Mulungu wanu anamulola kuti akhale wokanika+ ndi kuti aumitse mtima wake. Anatero kuti am’pereke m’manja mwanu monga mmene zilili lero.+ Salimo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+Chifukwa iwo akupandukirani.+ Miyambo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+ Amosi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa?
30 Koma Sihoni mfumu ya Hesiboni sanatilole kudutsa m’dziko lake, chifukwa Yehova Mulungu wanu anamulola kuti akhale wokanika+ ndi kuti aumitse mtima wake. Anatero kuti am’pereke m’manja mwanu monga mmene zilili lero.+
10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+Chifukwa iwo akupandukirani.+
21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+
6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa?