2 Samueli 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Abineri anayamba kufuulira Yowabu kuti: “Kodi tipitiriza kuphana ndi lupanga mpaka liti?+ Kodi sukudziwa kuti mapeto ake zimenezi zibweretsa mavuto aakulu?+ Kodi uwauza liti anthuwa kuti atembenuke ndi kusiya kutsatira abale awo?”+ Machitidwe 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lotsatira anaonekera kwa iwo pamene anali kumenyana, ndipo anayesa kuwayanjanitsa+ mwa kunena kuti, ‘Amuna inu, ndinu pachibale. N’chifukwa chiyani mukuzunzana chonchi?’+
26 Pamenepo Abineri anayamba kufuulira Yowabu kuti: “Kodi tipitiriza kuphana ndi lupanga mpaka liti?+ Kodi sukudziwa kuti mapeto ake zimenezi zibweretsa mavuto aakulu?+ Kodi uwauza liti anthuwa kuti atembenuke ndi kusiya kutsatira abale awo?”+
26 Tsiku lotsatira anaonekera kwa iwo pamene anali kumenyana, ndipo anayesa kuwayanjanitsa+ mwa kunena kuti, ‘Amuna inu, ndinu pachibale. N’chifukwa chiyani mukuzunzana chonchi?’+