Miyambo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+
14 Chiyambi cha mkangano chili ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.+ Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+