1 Mafumu 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova wati: “Musapite kukamenyana ndi abale anu, ana a Isiraeli.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake, chifukwa zimene zachitikazi, zachitika mwa kufuna kwanga.”’”+ Choncho anamvera mawu a Yehova+ n’kubwerera kwawo malinga ndi mawu a Yehova.+
24 ‘Yehova wati: “Musapite kukamenyana ndi abale anu, ana a Isiraeli.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake, chifukwa zimene zachitikazi, zachitika mwa kufuna kwanga.”’”+ Choncho anamvera mawu a Yehova+ n’kubwerera kwawo malinga ndi mawu a Yehova.+