1 Mafumu 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakati pa Asa ndi Basa mfumu ya Isiraeli pankachitika nkhondo masiku awo onse.+ 1 Mafumu 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano ine ndidzaseseratu Basa ndi nyumba yake, ndipo ndidzachititsa nyumba yake kukhala ngati nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati.+ 1 Mafumu 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Zimiri anafafaniza nyumba yonse ya Basa,+ malinga ndi mawu a Yehova+ otsutsana ndi Basa amene analankhula kudzera mwa Yehu mneneri.+ 2 Mbiri 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Pali pangano pakati pa ine ndi iwe, ndi pakati pa bambo anga ndi bambo ako. Taona, ndakutumizira siliva ndi golide. Pita ukaphwanye pangano lako ndi Basa+ mfumu ya Isiraeli kuti achoke kwa ine.”+
3 Tsopano ine ndidzaseseratu Basa ndi nyumba yake, ndipo ndidzachititsa nyumba yake kukhala ngati nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati.+
12 Choncho Zimiri anafafaniza nyumba yonse ya Basa,+ malinga ndi mawu a Yehova+ otsutsana ndi Basa amene analankhula kudzera mwa Yehu mneneri.+
3 “Pali pangano pakati pa ine ndi iwe, ndi pakati pa bambo anga ndi bambo ako. Taona, ndakutumizira siliva ndi golide. Pita ukaphwanye pangano lako ndi Basa+ mfumu ya Isiraeli kuti achoke kwa ine.”+