Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+ Salimo 109:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mbadwa zake ziphedwe ndi kuchotsedwa m’dziko.+Dzina lawo lifafanizidwe mu m’badwo wotsatira.+
5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+