Ekisodo 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero Farao, atumiki ake onse ndi Aiguputo onse anadzuka pakati pa usiku. Ndipo anthu anayamba kulira kwambiri m’dziko lonse la Iguputo,+ chifukwa panalibe banja ngakhale limodzi limene linalibe maliro. Salimo 76:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+
30 Zitatero Farao, atumiki ake onse ndi Aiguputo onse anadzuka pakati pa usiku. Ndipo anthu anayamba kulira kwambiri m’dziko lonse la Iguputo,+ chifukwa panalibe banja ngakhale limodzi limene linalibe maliro.
6 Hatchi komanso wokwera galeta agona tulo tofa nato chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Mulungu wa Yakobo.+