Deuteronomo 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwana wapathengo+ asalowe mumpingo wa Yehova. Ana ake asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10. Aheberi 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati simunalandire chilango chimene ena onse alandira, ndiye kuti ndinu ana apathengo,+ osati ana ake enieni.
2 “Mwana wapathengo+ asalowe mumpingo wa Yehova. Ana ake asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10.
8 Koma ngati simunalandire chilango chimene ena onse alandira, ndiye kuti ndinu ana apathengo,+ osati ana ake enieni.