Ekisodo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite chigololo.+ Levitiko 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+ Yohane 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.” Aheberi 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati simunalandire chilango chimene ena onse alandira, ndiye kuti ndinu ana apathengo,+ osati ana ake enieni.
10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+
41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.”
8 Koma ngati simunalandire chilango chimene ena onse alandira, ndiye kuti ndinu ana apathengo,+ osati ana ake enieni.