Yesaya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wodzikuza wochokera kufumbi adzawerama ndipo anthu odzikweza adzatsitsidwa.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+ Danieli 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndizo choonadi, njira zake ndi zolungama,+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+
17 Munthu wodzikuza wochokera kufumbi adzawerama ndipo anthu odzikweza adzatsitsidwa.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+
37 “Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndizo choonadi, njira zake ndi zolungama,+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+