Yeremiya 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo, ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.
16 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo, ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.