Ezekieli 34:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa ndidzawasandutsa dalitso.+ Ndidzagwetsa mvula yambiri pa nthawi yake. Kudzagwa mvula yambiri yamadalitso.+ Yakobo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho lezani mtima abale, kufikira kukhalapo*+ kwa Ambuye. Ganizirani mmene amachitira mlimi. Iye amayembekezerabe zipatso zofunika kwambiri zotuluka m’nthaka. Amakhala wodekha mpaka itagwa mvula yoyamba ndi mvula yomaliza.+
26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa ndidzawasandutsa dalitso.+ Ndidzagwetsa mvula yambiri pa nthawi yake. Kudzagwa mvula yambiri yamadalitso.+
7 Choncho lezani mtima abale, kufikira kukhalapo*+ kwa Ambuye. Ganizirani mmene amachitira mlimi. Iye amayembekezerabe zipatso zofunika kwambiri zotuluka m’nthaka. Amakhala wodekha mpaka itagwa mvula yoyamba ndi mvula yomaliza.+