Ezekieli 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+ Ezekieli 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
16 “Nkhosa zosochera ndidzazifunafuna,+ zomwazika ndidzazibweza. Yothyoka mwendo ndidzaimanga mwendo wothyokawo. Yodwala ndidzailimbitsa, koma yonenepa+ ndi yamphamvu ndidzaiwononga. Ndidzaipatsa chiweruzo monga chakudya chake.”+
17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+