Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 19:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma mmodzi wa asilikaliwo anamulasa ndi mkondo m’mbalimu cham’mimba,+ ndipo nthawi yomweyo panatuluka magazi ndi madzi.

  • Yohane 19:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiponso lemba lina limati: “Iwo adzayang’ana kwa munthu amene anamulasa.”+

  • Yohane 20:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako anauza Tomasi kuti: “Ika chala chako apa, ndiponso ona m’manja mwangamu. Gwiranso ndi dzanja lako+ m’mbali mwa mimba yangamu, kuti usakhalenso wosakhulupirira, koma wokhulupirira.”

  • Chivumbulutso 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Taonani! Akubwera ndi mitambo,+ ndipo diso lililonse lidzamuona,+ ngakhalenso anthu amene anamulasa.+ Ndipo mafuko onse a padziko lapansi adzadziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye.+ Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena