Machitidwe 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.
23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.