Yesaya 43:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Koma iwe Yakobo, iwe Isiraeli, sunapemphe thandizo kwa ine+ chifukwa chakuti watopa nane.+ Mika 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu anthu anga,+ ndakulakwirani chiyani? Kodi ndakutopetsani mwa njira yanji?+ Perekani umboni wonditsutsa.+
3 “Inu anthu anga,+ ndakulakwirani chiyani? Kodi ndakutopetsani mwa njira yanji?+ Perekani umboni wonditsutsa.+