Yesaya 64:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Palibe amene akutamanda dzina lanu.+ Palibe amene akutekeseka kuti akufunefuneni ndi kukugwirani mwamphamvu, pakuti mwatibisira nkhope yanu+ ndipo mwatichititsa kuti tisungunuke+ ndi mphamvu ya zolakwa zathu.
7 Palibe amene akutamanda dzina lanu.+ Palibe amene akutekeseka kuti akufunefuneni ndi kukugwirani mwamphamvu, pakuti mwatibisira nkhope yanu+ ndipo mwatichititsa kuti tisungunuke+ ndi mphamvu ya zolakwa zathu.