Yeremiya 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mneneri amene walosera za mtendere+ amadziwika kuti ndi munthu amene Yehova wamutumadi ulosi wakewo ukakwaniritsidwa.”+ Ezekieli 33:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+
9 Koma mneneri amene walosera za mtendere+ amadziwika kuti ndi munthu amene Yehova wamutumadi ulosi wakewo ukakwaniritsidwa.”+
33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+