Mateyu 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malemba amanena za iyeyu kuti, ‘Taona! Inetu ndikutumiza mthenga wanga choyamba, amene adzakukonzera njira!’+ Luka 1:76 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 76 Koma kunena za iwe, mwanawe, udzatchedwa mneneri wa Wam’mwambamwamba, pakuti udzatsogola pamaso pa Yehova kuti ukakonzeretu njira zake.+ Yohane 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panaonekera munthu wina amene anatumidwa monga nthumwi ya Mulungu.+ Dzina lake anali Yohane.+
10 Malemba amanena za iyeyu kuti, ‘Taona! Inetu ndikutumiza mthenga wanga choyamba, amene adzakukonzera njira!’+
76 Koma kunena za iwe, mwanawe, udzatchedwa mneneri wa Wam’mwambamwamba, pakuti udzatsogola pamaso pa Yehova kuti ukakonzeretu njira zake.+