Danieli 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ena mwa anthu ozindikirawo adzapunthwa.+ Zidzatero kuti ntchito yoyenga ichitike* ndiponso kuti anthu ozindikira atsukidwe ndi kuyeretsedwa+ kufikira nthawi ya mapeto,+ pakuti nthawi yake idzafika.+ Danieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+ 1 Akorinto 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.
35 Ena mwa anthu ozindikirawo adzapunthwa.+ Zidzatero kuti ntchito yoyenga ichitike* ndiponso kuti anthu ozindikira atsukidwe ndi kuyeretsedwa+ kufikira nthawi ya mapeto,+ pakuti nthawi yake idzafika.+
10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+
13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.