Maliko 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake anam’tumizira ena mwa Afarisi ndi a chipani cha Herode,+ kuti akam’kole m’mawu ake.+ Luka 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, n’cholinga choti akamukole+ m’mawu ake, kuti akamupereke ku boma ndi kwa bwanamkubwa.+
20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, n’cholinga choti akamukole+ m’mawu ake, kuti akamupereke ku boma ndi kwa bwanamkubwa.+