Luka 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho iwo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti mumanena ndi kuphunzitsa molondola ndipo mulibe tsankho, koma mumaphunzitsa njira ya Mulungu mogwirizana ndi choonadi.+ Yohane 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyeyu anabwera kwa Yesu usiku+ ndi kumuuza kuti: “Rabi,+ tikudziwa kuti inu ndinu mphunzitsi+ wochokera kwa Mulungu,+ chifukwa munthu sangathe kuchita zizindikiro+ zimene inu mumachita ngati Mulungu sali naye.”+
21 Choncho iwo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti mumanena ndi kuphunzitsa molondola ndipo mulibe tsankho, koma mumaphunzitsa njira ya Mulungu mogwirizana ndi choonadi.+
2 Iyeyu anabwera kwa Yesu usiku+ ndi kumuuza kuti: “Rabi,+ tikudziwa kuti inu ndinu mphunzitsi+ wochokera kwa Mulungu,+ chifukwa munthu sangathe kuchita zizindikiro+ zimene inu mumachita ngati Mulungu sali naye.”+