Luka 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo iwo analephera kumutapa m’kamwa pa zimene ananenazi pamaso pa anthu, mwakuti pothedwa nzeru ndi yankho lake, anangokhala chete kusowa chonena.+
26 Pamenepo iwo analephera kumutapa m’kamwa pa zimene ananenazi pamaso pa anthu, mwakuti pothedwa nzeru ndi yankho lake, anangokhala chete kusowa chonena.+