Maliko 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi pouka kwa akufa mkazi ameneyu adzakhala wa ndani? Popeza onse 7 anam’kwatira.”+ Luka 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi pamenepa, pouka kwa akufa, mkazi ameneyu adzakhala wa ndani popeza onse 7 anamukwatira?”+