Mateyu 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi pamenepa, pouka kwa akufa, mkazi ameneyu adzakhala wa ndani popeza onse 7 anamukwatira?”+ Luka 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi pamenepa, pouka kwa akufa, mkazi ameneyu adzakhala wa ndani popeza onse 7 anamukwatira?”+