Luka 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako munthu wina wodziwa Chilamulo+ anaimirira kuti amuyese. Iye anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, ndizichita chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+
25 Kenako munthu wina wodziwa Chilamulo+ anaimirira kuti amuyese. Iye anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, ndizichita chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+