Mateyu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano munthu wina anafika kwa iye ndi kumufunsa kuti: “Mphunzitsi, n’chiyani chabwino chimene ndiyenera kuchita kuti ndikapeze moyo wosatha?”+ Maliko 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano pamene anali kupita, mwamuna wina anam’thamangira ndi kugwada pamaso pake. Kenako anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndichite chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+ Luka 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano wolamulira wina anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndizichita chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+
16 Tsopano munthu wina anafika kwa iye ndi kumufunsa kuti: “Mphunzitsi, n’chiyani chabwino chimene ndiyenera kuchita kuti ndikapeze moyo wosatha?”+
17 Tsopano pamene anali kupita, mwamuna wina anam’thamangira ndi kugwada pamaso pake. Kenako anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndichite chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+
18 Tsopano wolamulira wina anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndizichita chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+