Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 19:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Aliyense amene wasiya nyumba, abale, alongo, abambo, amayi, ana kapena minda chifukwa cha dzina langa adzalandira zochuluka kwambiri kuposa zimenezi, ndipo adzapeza moyo wosatha.+

  • Maliko 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano pamene anali kupita, mwamuna wina anam’thamangira ndi kugwada pamaso pake. Kenako anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndichite chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+

  • Luka 10:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako munthu wina wodziwa Chilamulo+ anaimirira kuti amuyese. Iye anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, ndizichita chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+

  • Luka 18:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano wolamulira wina anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndizichita chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena