Maliko 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano mmodzi wa alembi amene anafika ndi kuwamva akutsutsana, anadziwa kuti anawayankha bwino, ndipo anafunsa Yesu kuti: “Kodi lamulo loyamba ndi liti pa malamulo onse?”+
28 Tsopano mmodzi wa alembi amene anafika ndi kuwamva akutsutsana, anadziwa kuti anawayankha bwino, ndipo anafunsa Yesu kuti: “Kodi lamulo loyamba ndi liti pa malamulo onse?”+