Aroma 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi+ sichilimbikitsa munthu kuchitira zoipa mnzake,+ chotero chilamulo chimakwaniritsidwa m’chikondi.+ Agalatiya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Chilamulo chonse chimakwaniritsidwa+ m’mawu akuti: “Uzikonda mnzako ngati mmene umadzikondera wekha.”+
10 Chikondi+ sichilimbikitsa munthu kuchitira zoipa mnzake,+ chotero chilamulo chimakwaniritsidwa m’chikondi.+
14 Pakuti Chilamulo chonse chimakwaniritsidwa+ m’mawu akuti: “Uzikonda mnzako ngati mmene umadzikondera wekha.”+