Maliko 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Davideyo anamutcha kuti ‘Ambuye,’ nanga zikutheka bwanji kuti alinso mwana wake?”+ Ndipo khamu lalikulu linali kumumvetsera mosangalala.+
37 Davideyo anamutcha kuti ‘Ambuye,’ nanga zikutheka bwanji kuti alinso mwana wake?”+ Ndipo khamu lalikulu linali kumumvetsera mosangalala.+