Maliko 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Komanso amakonda kukhala m’mipando yakutsogolo m’masunagoge. Amakondanso malo olemekezeka kwambiri pa chakudya chamadzulo.+ Luka 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ataona mmene anthu oitanidwawo anali kusankhira malo olemekezeka kwambiri, anawauza fanizo kuti:+ Luka 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni,+ kuti munthu amene wakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Pamenepo udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+
39 Komanso amakonda kukhala m’mipando yakutsogolo m’masunagoge. Amakondanso malo olemekezeka kwambiri pa chakudya chamadzulo.+
10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni,+ kuti munthu amene wakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Pamenepo udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+