Deuteronomo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mukawoloka Yorodano, muimike miyala imeneyi paphiri la Ebala,+ monga mmene ndakulamulirani lero, ndipo muipake utoto woyera.+ Luka 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Tsoka inu, chifukwa muli ngati manda achikumbutso osaonekera, moti anthu amayenda pamwamba pake koma osadziwa!”+ Machitidwe 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Paulo anamuuza kuti: “Uona, Mulungu akukantha, khoma* lopaka laimu+ iwe. Wakhala pamenepo kuti undiweruze motsatira Chilamulo,+ kodi ukuphwanyanso wekha Chilamulocho+ polamula kuti andimenye?”
4 Choncho mukawoloka Yorodano, muimike miyala imeneyi paphiri la Ebala,+ monga mmene ndakulamulirani lero, ndipo muipake utoto woyera.+
44 Tsoka inu, chifukwa muli ngati manda achikumbutso osaonekera, moti anthu amayenda pamwamba pake koma osadziwa!”+
3 Pamenepo Paulo anamuuza kuti: “Uona, Mulungu akukantha, khoma* lopaka laimu+ iwe. Wakhala pamenepo kuti undiweruze motsatira Chilamulo,+ kodi ukuphwanyanso wekha Chilamulocho+ polamula kuti andimenye?”