2 Mbiri 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamapeto pake anthuwo anam’konzera chiwembu+ ndipo anam’ponya miyala+ pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu. Yohane 8:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pamenepo anatola miyala kuti amugende nayo,+ koma Yesu anabisala ndi kutuluka m’kachisimo. 1 Atesalonika 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.
21 Pamapeto pake anthuwo anam’konzera chiwembu+ ndipo anam’ponya miyala+ pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu.
15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.