Aheberi 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+
36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+