Maliko 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno adzatumiza angelo ndipo adzasonkhanitsa pamodzi osankhidwa+ ake kuchokera kumphepo zinayi, kuchokera kumalekezero ake a dziko lapansi kukafika kumalekezero a m’mlengalenga.+
27 Ndiyeno adzatumiza angelo ndipo adzasonkhanitsa pamodzi osankhidwa+ ake kuchokera kumphepo zinayi, kuchokera kumalekezero ake a dziko lapansi kukafika kumalekezero a m’mlengalenga.+